Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 August tsamba 7
  • August 29–September 4

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 29–September 4
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 August tsamba 7

August 29–September 4

MASALIMO 110-118

  • Nyimbo Na. 61 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Yehova Ndidzamubwezera Chiyani?”: (10 min.)

    • Sal. 116:3, 4, 8—Yehova anathandiza wolemba Masalimo kuti asaphedwe (w87-E 3/15 24 ndime 5; w09 7/15 29 ndime 4 )

    • Sal. 116:12—Wolemba Masalimo anatsimikiza mtima kumuthokoza Yehova chifukwa cha zimene anamuchitira (w09 7/15 29 ndime 4-5; w98 12/1 24 ndime 3)

    • Sal. 116:13, 14, 17, 18—Wolemba Masalimoyu ankayesetsa kuchita zonse zimene Mulungu amafuna komanso kukwaniritsa zinthu zonse zimene anamulonjeza (w10 4/15 27, komanso bokosi)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Sal. 110:4—Kodi palembali mawu akuti ‘kulumbira’ akutanthauza chiyani? (w14 10/15 11 ndime 15-17; w06 9/1 14 ndime 1)

    • Sal. 116:15—Pokamba nkhani ya maliro, n’chifukwa chiyani vesili siliyenera kugwiritsidwa ntchito ponena za munthu amene wamwalirayo? (w12 5/15 22 ndime 2)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 110:1–111:10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) ll 16—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) ll 17—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 179-181 ndime 17-19—Muthandizeni wophunzirayo kuti aone mmene angagwiritsire ntchito mfundo za m’ndimezi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 82

  • “Kuphunzitsa Choonadi”: (7 min.) Nkhani yokambirana.

  • “Tidzagwira Ntchito Yapadera Yogawira Nsanja ya Olonda mu September”: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yosonyeza chitsanzo choyamba chogawira magazini m’mwezi wa September ndipo kenako kambiranani zomwe mwaona m’vidiyoyo. Limbikitsani anthu kuti adzagwire nawo ntchitoyi komanso kuti adzachite nawo upainiya wothandiza.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 5 ndime 14-26, komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 50.

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 144 ndi Pemphero

    Kumbukirani kuti, muyenera kuika nyimboyi kuti onse aimvetsere kenako muibwerezenso kuti onse aimbe nawo.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena