Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 September tsamba 4
  • “Thandizo Langa Lichokera kwa Yehova”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Thandizo Langa Lichokera kwa Yehova”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Nkhani Yofanana
  • Mulungu Wachimwemwe, Anthu Achimwemwe!
    Nsanja ya Olonda—1987
  • Mfundo Zazikulu za Chigawo Chachisanu cha Masalmo
    Nsanja ya Olonda—2006
  • Nyimbo Zouziridwa Zomwe Ndi Zolimbikitsa Komanso Zamalangizo
    Kodi Baibulo Lili Ndi Uthenga Wotani?
  • Mafunso Ochokera kwa Oŵerenga
    Nsanja ya Olonda—2003
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 September tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 120-134

“Thandizo Langa Lichokera kwa Yehova”

Masalimo 120 mpaka 134 amadziwikanso kuti nyimbo zokwerera kumzinda. Anthu ena amakhulupirira kuti Masalimowa ankaimbidwa ndi anthu amene ankapita ku Yerusalemu kukalambira Mulungu. Amakhulupirira kuti anthuwa ankadutsa m’mapiri a ku Yuda akamapita ku zikondwerero za pachaka.

Aisiraeli akupita ku Yerusalemu

Masalimowa amayerekezera chitetezo cha Yehova ndi . . .

121:3-8

  • M’busa

    M’busa amene ali maso

  • Mtengo umapereka mthunzi

    Mthunzi

  • Asilikali

    Msilikali wokhulupirika

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena