Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 November tsamba 6
  • November 21-27

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 21-27
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 November tsamba 6

November 21-27

MLALIKI 7-12

  • Nyimbo Na. 41 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kumbukira Mlengi Wako Wamkulu Masiku a Unyamata Wako”: (10 min.)

    • Mlal. 12:1—Achinyamata ayenera kugwiritsa ntchito nthawi ndi mphamvu zawo potumikira Mulungu (w14 1/15 18 ndime 3; w14 1/15 22 ndime 1)

    • Mlal. 12:2-7—Achinyamata angachite zambiri chifukwa sakhala ndi mavuto amene anthu okalamba amakumana nawo (w08 11/15 23 ndime 2; w06 11/1 16 ndime 9)

    • Mlal. 12:13, 14—Kutumikira Yehova n’kumene kungakuthandizeni kukhala osangalala (w11 11/1 21 ndime 1-6)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Mlal. 10:1—Kodi “uchitsiru pang’ono” ungawononge bwanji mbiri ya munthu? (w06 11/1 16 ndime 5)

    • Mlal. 11:1—Kodi ‘kutumiza mkate wako pamadzi’ kumatanthauza chiyani? (w06 11/1 16 ndime 7)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mlal. 10:12-20; 11:1-10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) 2 Tim. 3:1-5—Kuphunzitsa Choonadi.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yes. 44:27-28; 45:1-2—Kuphunzitsa Choonadi.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 26 ndime 18-20—Muitanireni munthuyo kumisonkhano yathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 95

  • “Achinyamata Musachedwe Kulowa ‘Pakhomo Lalikulu’”: (15 min.) Onetsani vidiyo yakuti Achinyamata—Yehova Amakukondani Kwambiri. (Imapezeka pa tv.jw.org/ny pamene palembedwa kuti MISONKHANO NDI UTUMIKI WATHU.) Kenako kambiranani nkhaniyi.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 11 ndime 12-20 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 98.

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 148 ndi Pemphero

    Kumbukirani: Muyenera kuika nyimboyi kuti onse amvetsere, kenako muibwerezenso kuti onse aimbe nawo.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena