Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 January tsamba 2
  • January 2-8

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 2-8
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 January tsamba 2

January 2-8

YESAYA 24-28

  • Nyimbo Na. 12 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Amasamalira Anthu Ake”: (10 min.)

    • Yes. 25:4, 5—Yehova ndi malo achitetezo kwa anthu onse amene amamutumikira (ip-1 272 ¶5)

    • Yes. 25:6—Yehova akukwaniritsa zimene analonjeza zoti adzatipatsa chakudya chochuluka chauzimu (w16.5 24 ¶4; ip-1 273 ¶6-7)

    • Yes. 25:7, 8—Posachedwapa uchimo ndi imfa sizikhalaponso (w14 9/15 26 ¶15; ip-1 273-274 ¶8-9)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yes. 26:15—Kodi tingathandize bwanji Yehova pamene ‘akufutukulira kutali malire onse a dzikoli’? (w15 7/15 11 ¶18)

    • Yes. 26:20—Kodi zikuoneka kuti ‘zipinda zamkati’ zikuimira chiyani? (w13 3/15 23 ¶15-16)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 28:1-13

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Nkhani yokambirana. Pambuyo poonetsa vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki iliyonse, kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’vidiyoyo. Dziwani izi: Palibe vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki wa kapepala kakuti Kodi Mukufuna Kudziwa Choonadi? Choncho pemphani ofalitsa awiri kuti achite chitsanzo cha mmene tingagawirire kapepalaka.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 138

  • Zofunika Pampingo: (15 min.) Mukhoza kukambirana zimene tikuphunzira mu Buku Lapachaka. (yb16 140-142)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 14 ¶14-22 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 124

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 66 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena