Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 January tsamba 4
  • January 16-22

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 16-22
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 January tsamba 4

January 16-22

YESAYA 34-37

  • Nyimbo Na. 31 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Hezekiya Anadalitsidwa Chifukwa cha Chikhulupiriro Chake”: (10 min.)

    • Yes. 36:1, 4-10, 15, 18-20—Asuri ankanyoza Yehova ndiponso kuopseza anthu ake (ip-1 385-388 ¶7-14)

    • Yes. 37:1, 2, 14-20—Hezekiya anadalira Yehova (ip-1 388-391 ¶15-17)

    • Yes. 37:33-38—Yehova anateteza anthu ake (ip-1 391-394 ¶18-22)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yes. 35:8—Kodi “Msewu wa Chiyero” unali chiyani, nanga ndi ndani amene ankayenera kuyendamo? (w08 5/15 26 ¶4; 27 ¶1)

    • Yes. 36:2, 3, 22—Kodi Sebina anasonyeza bwanji chitsanzo chabwino atachotsedwa pa udindo? (w07 1/15 9 ¶1)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 36:1-12

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Mat. 24:3, 7, 14—Kuphunzitsa Choonadi—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) 2 Tim. 3:1-5—Kuphunzitsa Choonadi—Musiyireni khadi lodziwitsa anthu za JW.ORG.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 33 ¶11-12—Muitanireni kumisonkhano.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 91

  • “Inu Yehova, . . . Chikhulupiriro Changa Chili mwa Inu”: (15 min.) Mafunso ndi mayankho. Yambani ndi kuonetsa vidiyo yakuti “Inu Yehova, . . . Chikhulupiriro Changa Chili mwa Inu”—Kachigawo Kochepa.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 15 ¶15-26 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 134

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 96 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena