CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 8-11
Anthu Akamatsogoleredwa ndi Yehova Zinthu Zimawayendera Bwino
Anthu alibe luso komanso ufulu woti azidzilamulira okha
Aisiraeli anabalalika chifukwa choti abusa awo sankafunafuna Yehova
Anthu amene ankatsatira malangizo a Yehova anali pa mtendere, ankakhala mosangalala komanso zinthu zinkawayendera bwino