Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 April tsamba 6
  • April 17-23

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 17-23
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 April tsamba 6

April 17-23

YEREMIYA 25-28

  • Nyimbo Na. 137 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Khalani Olimba Mtima Ngati Yeremiya”: (10 min.)

    • Yer. 26:2-6​—Yehova anatuma Yeremiya kuti alengeze uthenga wochenjeza anthu (w09 12/1 24 ¶6)

    • Yer. 26:8, 9, 12, 13​—Yeremiya sanaope anthu amene ankadana naye (jr 21 ¶13)

    • Yer. 26:16, 24​—Yehova anateteza mneneri wake wolimba mtimayu (w09 12/1 25 ¶1)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yer. 27:2, 3​—Kodi n’chifukwa chiyani amithenga ochokera m’mitundu yosiyanasiyana anabwera ku Yerusalemu, nanga n’chifukwa chiyani Yeremiya anawapangira magoli? (jr 27 ¶21)

    • Yer. 28:11​—Kodi Yeremiya anachita bwanji zinthu mwanzeru pamene Hananiya ankamutsutsa, ndipo tikuphunzira chiyani pa chitsanzo chakechi? (jr 187-188 ¶11-12)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer. 27:12-22

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) T-36​—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) T-36​—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 7 ¶4-5​—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 17

  • “Nyimbo za Ufumu Zimatithandiza Kuti Tikhale Olimba Mtima”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Nyimbo Imene Inalimbikitsa Akaidi.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 22 ¶1-13

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 26 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena