CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 49-50
Yehova Amadalitsa Anthu Odzichepetsa Ndipo Amalanga Odzikuza
Aisiraeli omwe analapa anasangalala Yehova atawamasula ku ukapolo
Iwo anabwerezanso pangano lawo lomwe anachita ndi Yehova ndipo anabwerera ku Yerusalemu n’kukayambiranso kulambira Mulungu
Ababulo omwe anali odzikuza, analangidwa chifukwa ankachitira nkhanza anthu a Yehova
Monga mmene ulosi unanenera, Babulo anakhala bwinja