Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 August tsamba 6
  • August 21-27

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 21-27
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 August tsamba 6

August 21-27

EZEKIELI 35-38

  • Nyimbo Na. 132 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Gogi wa ku Magogi Awonongedwa Posachedwapa”: (10 min.)

    • Ezek. 38:2​—Dzina loti Gogi wa ku Magogi likuimira mgwirizano wa mitundu ya anthu (w15 5/15 29-30)

    • Ezek. 38:14-16​—Gogi wa ku Magogi adzaukira atumiki a Yehova (w12 9/15 5-6 ¶8-9)

    • Ezek. 38:21-23​—Yehova Mulungu adzazilemekeza komanso kudziyeretsa powononga Gogi wa ku Magogi (w14 11/15 27 ¶16)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Ezek. 36:20, 21​—Kodi chifukwa chachikulu chimene timafunikira kukhala ndi makhalidwe abwino ndi chiti? (w02 6/15 20 ¶12)

    • Ezek. 36:33-36​—Kodi mawu a mu vesili akukwaniritsidwa bwanji masiku ano? (w88 9/15 24 ¶11)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 35:1-15

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Sal. 37:29​—Kuphunzitsa Choonadi.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Gen. 1:28; Yes. 55:11​—Kuphunzitsa Choonadi.

  • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w16.07 31-32​—Mutu: Kodi Zimene Ezekieli Anauzidwa Kuti Aphatikize Ndodo Ziwiri N’kukhala Imodzi Zikuimira Chiyani?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 54

  • “Muzikhala ndi Makhalidwe Amene Mulungu Amasangalala Nawo​—Chikhulupiriro”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Muzichita Zinthu Zimene Zingakulimbikitseni Kukhala Okhulupirika​—Chikhulupiriro.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 5 ¶18-25 komanso tsamba 57

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 119 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena