November 13-19
OBADIYA 1–YONA 4
Nyimbo Na. 42 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muziphunzirapo Kanthu pa Zimene Munalakwitsa”: (10 min.)
[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Obadiya.]
[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Yona.]
Yona 3:1-3—Yona anaphunzirapo kanthu pa zimene analakwitsa (ia 114 ¶22-23)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Obad. 10—Kodi mawu akuti Edomu ‘sadzakhalaponso mpaka kalekale’ anakwaniritsidwa bwanji? (w07 11/1 13 ¶5)
Obad. 12—Kodi tikuphunzirapo chiyani pa zimene Mulungu ananena podzudzula Aedomu? (jd 112 ¶4-5)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yona 3:1-10
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) wp17.6 chikuto—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) wp17.6 chikuto—Pitirizani kukambirana zokhudza magazini imene munamupatsa kale. Musonyezeni limodzi mwa mabuku amene timagwiritsa ntchito pophunzira Baibulo.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) ld 12-13—Sankhani zithunzi zoti mukambirane.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Zimene Tikuphunzira Kuchokera m’Buku la Yona”: (15 min.) Yambani ndi kuonetsa vidiyo yakuti Kulambira kwa Pabanja: Yona Anaphunzirapo Kanthu pa Chifundo cha Yehova.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 10 ¶1-7 komanso tsamba 98 ndi 99
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 133 ndi Pemphero