Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 April tsamba 3
  • April 9-15

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 9-15
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 April tsamba 3

April 9-15

MATEYU 27-28

  • Nyimbo Na. 69 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Tingamvere Bwanji Lamulo Lakuti, Pitani Mukaphunzitse Anthu?”: (10 min.)

    • Mat. 28:18​—Yesu ali ndi ulamuliro waukulu (w04 7/1 8 ¶4)

    • Mat. 28:19​—Yesu anayambitsa ntchito yapadziko lonse yolalikira komanso kuphunzitsa (“mukaphunzitse” “anthu a mitundu yonse” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 28:19, nwtsty)

    • Mat. 28:20​—Tiyenera kuphunzitsa anthu komanso kuwathandiza kuti azitsatira zonse zimene Yesu anaphunzitsa (“ndi kuwaphunzitsa” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 28:20, nwtsty)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Mat. 27:51​—Kodi kung’ambika pakati kwa nsalu yotchinga kunkaimira chiyani? (“nsalu yotchinga” “m’nyumba yopatulika” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 27:51, nwtsty)

    • Mat. 28:7​—Kodi mngelo wa Yehova anasonyeza bwanji kuti analemekeza azimayi omwe anapita kumanda a Yesu? (“mukauze ophunzira ake kuti wauka” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 28:7, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mat. 27:38-54

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) g17.2 14​—Mutu: Kodi Yesu Anafera Pamtanda?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 70

  • “Kulalikira Komanso Kuphunzitsa N’kofunika Kwambiri Kuti Tipange Ophunzira”: (15 min.) Nkhani Yokambirana. Pokambirana nkhaniyi, onetsani vidiyo yakuti, Pitirizani Kulalikira “Mwakhama”​—Mwamwayi Komanso Kunyumba ndi Nyumba komanso yakuti, Pitirizani Kulalikira “Mwakhama”​—M’malo Opezeka Anthu Ambiri Komanso Muzithandiza Anthu Kuti Akhale Ophunzira a Yesu.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 16 ¶6-17

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 73 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena