Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 April tsamba 5
  • April 23-29

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 23-29
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 April tsamba 5

April 23-29

MALIKO 3-4

  • Nyimbo Na. 77 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Anachiritsa Munthu pa Tsiku la Sabata”: (10 min.)

    • Maliko 3:1, 2​—Atsogoleri achipembedzo achiyuda ankafuna kumupezera Yesu chifukwa chomuimbira mlandu (jy 78 ¶1-2)

    • Maliko 3:3, 4​—Yesu anadziwa kuti atsogoleriwo ankakhwimitsa kwambiri malamulo okhudza Sabata (jy 78 ¶3)

    • Maliko 3:5​—Yesu anamva “chisoni kwambiri chifukwa cha kuuma mtima kwawo” (“mokwiya ndi kumva chisoni kwambiri” mfundo zimene ndikuphunzira pa maliko 3:5, nwtsty)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Maliko 3:28, 29​—Kodi kunyoza mzimu woyera kumatanthauza chiyani, ndipo zotsatira zake zimakhala zotani? (“wanyoza mzimu woyera” “mlandu wa tchimo losatha” mfundo zimene ndikuphunzira pa maliko 3:29, nwtsty)

    • Maliko 4:26-29​—Kodi tikuphunzira chiyani pa fanizo la Yesu la wofesa mbewu amene amagona usiku n’kumadzuka kukacha? (w14 12/15 12-13 ¶6-8)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Maliko 3:1-19a

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse ndipo gawirani buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 36 ¶21-22​—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 103

  • “Amene Ali ndi Makutu Akumva, Amve”: (15 min.) Fotokozani zimene lemba la Maliko 4:9 limatanthauza (“Amene ali ndi makutu akumva, amve” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 4:9, nwtsty). Onerani vidiyo yakuti Mukamamvera Uphungu Mudzakhala Anzeru. Kenako kambiranani bokosi lakuti “Mvera Uphungu Ndipo Utsatire Malangizo” m’mutu 4, m’buku lakuti Kodi Mungatani Kuti ‘Mulungu Apitirize Kukukondani?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 17 ¶1-9

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena