Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 April tsamba 6
  • April 30–May 6

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 30–May 6
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 April tsamba 6

April 30–May 6

MALIKO 5-6

  • Nyimbo Na. 151 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yesu Ali ndi Mphamvu Zoukitsa Anthu Amene Anamwalira”: (10 min.)

    • Maliko 5:38​—Timalira munthu amene timam’konda akamwalira

    • Maliko 5:39-41​—Yesu ali ndi mphamvu zoukitsa anthu amene “akugona” mu imfa (“sanamwalire ayi, koma akugona” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 5:39, nwtsty)

    • Maliko 5:42​—‘Tidzasangalala kwambiri’ anthu akamadzaukitsidwa m’tsogolo (jy 118 ¶6)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Maliko 5:19, 20​—N’chifukwa chiyani Yesu pa nthawiyi anapereka malangizo osiyana ndi omwe ankapereka nthawi zonse? (“ukawauze” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 5:19, nwtsty)

    • Maliko 6:11​—Kodi mawu akuti “sansani fumbi kumapazi anu” amatanthauza chiyani? (“sansani fumbi kumapazi anu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 6:11, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Maliko 6:1-13

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene. Musonyezeni webusaiti ya jw.org.

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse loti mugwiritse ntchito komanso funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 36 ¶23-24​—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 144

  • “Tizigwiritsa Ntchito Mwaluso Zinthu Zomwe Timagwiritsa Ntchito Pophunzitsa”: (5 min.) Nkhani yokambirana.

  • Timatonthozedwa Chifukwa Chokhala M’gulu la Yehova: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyoyi. Kenako kambiranani mafunso otsatirawa: Kodi banja la a Pera linakumana ndi mavuto otani? N’chiyani chinawathandiza kuti apirire? Kodi n’chifukwa chiyani tiyenera kupitirizabe kuchita zinthu zokhudza kulambira ngakhale pamene takumana ndi mayesero?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 17 ¶10-18

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 72 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena