Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 May tsamba 6
  • May 28–June 3

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 28–June 3
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 May tsamba 6

May 28–June 3

MALIKO 13-14

  • Nyimbo Na. 55 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Pewani Msampha Woopa Anthu”: (10 min.)

    • Maliko 14:29, 31​—Atumwi sankafuna kumukana Yesu

    • Maliko 14:50​—Pamene Yesu anamangidwa, atumwi ake onse anamuthawa

    • Maliko 14:47, 54, 66-72​—Petulo analimba mtima kuti ateteze Yesu moti ankamutsatira chapatali, koma kenako anamukana katatu (ia 200 ¶14; it-2 619 ¶6)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Maliko 14:51, 52​—Kodi mnyamata amene anathawa ali malisecheyu ayenera kuti anali ndani? (w08 2/15 30 ¶6)

    • Maliko 14:60-62​—Kodi n’kutheka kuti Yesu anasankha kuyankha funso la mkulu wa ansembe chifukwa chiyani? (jy 287 ¶4)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Maliko 14:43-59

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene. Muitanireni kumisonkhano yathu.

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba limene mukufuna kugwiritsira ntchito. M’patseni buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 181-182 ¶17-18

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 73

  • “Yehova Akuthandiza Kuti Ukhale Wolimba Mtima”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 19 ¶1-7 komanso tsamba 203, 204-205

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 81 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena