Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 June tsamba 4
  • June 11-17

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 11-17
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 June tsamba 4

June 11-17

Luka 1

  • Nyimbo Na. 137 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzitsanzira Mariya Pokhala Odzichepetsa”: (10 min.)

    • [Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Luka.]

    • Luka 1:38​—Mariya anavomera modzichepetsa kugwira ntchito imene Mulungu anamupatsa (ia 149 ¶12)

    • Luka 1:46-55​—Iye anatamanda Yehova pofotokoza mfundo zochokera m’Mawu a Mulungu (ia 151 ¶15-16)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Luka 1:69​—Kodi mawu akuti “nyanga yachipulumutso” amatanthauza chiyani? (“nyanga yachipulumutso” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 1:69, nwtsty)

    • Luka 1:76​—Kodi Yohane M’batizi ‘anatsogola pamaso pa Yehova’ m’njira yotani? (“anatsogola pamaso pa Yehova” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 1:76, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 1:46-66

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 92

  • Zofunika Pampingo: (8 min.) Mukhoza kukambirana mfundo zokhudza lemba la chaka cha 2018. (w18.01 8-9 ¶4-7)

  • Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onerani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lathu Lachita ya June.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 20 ¶1-6 komanso tsamba 211, 214-215

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 58 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena