Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 June tsamba 5
  • June 18-24

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 18-24
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 June tsamba 5

June 18-24

Luka 2-3

  • Nyimbo Na. 133 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Ananu, Kodi Mukuyesetsa Kuti Yehova Akhale Mnzanu Wapamtima?”: (10 min.)

    • Luka 2:41, 42​—Yesu anapita kumwambo wapachaka wa Pasika ndi makolo ake (“makolo ake anali kukonda” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 2:41, nwtsty)

    • Luka 2:46, 47​—Yesu anamvetsera komanso kufunsa mafunso atsogoleri achipembedzo (“kuwafunsa mafunso” “anadabwa kwambiri” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 2:46, 47, nwtsty)

    • Luka 2:51, 52​—Yesu ‘anapitiriza kumvera’ makolo ake ndipo Mulungu ndi anthu ankakondwera naye (“anapitiriza kuwamvera” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 2:51, 52, nwtsty)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Luka 2:14​—Kodi vesi limeneli likutanthauza chiyani? (“ndipo pansi pano mtendere pakati pa anthu amene iye amakondwera nawo” “anthu amene iye amakondwera nawo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 2:14, nwtsty)

    • Luka 3:23​—Kodi bambo ake a Yosefe anali ndani kwenikweni? (wp16.3 9 ¶1-3)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 2:1-20

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Yambani ndi chitsanzo cha zimene tinganene. Kenako sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri.

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w14 2/15 26-27​—Mutu: N’chifukwa Chiyani Ayuda a M’nthawi ya Yohane Mbatizi “Anali Kuyembekezera” Mesiya?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 134

  • “Makolo, Muzithandiza Ana Anu Kuti Azikonda Kwambiri Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Anagwiritsa Ntchito Mwayi Umene Anali Nawo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 20 ¶7-16 komanso tsamba 215

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 17 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena