July 2-8
Luka 6-7
Nyimbo Na. 109 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzikhala Owolowa Manja”: (10 min.)
Luka 6:37—Ngati tikufuna kuti anthu ena azitikhululukira, ifenso tizikhululuka (“Pitirizani kukhululukira anthu machimo awo ndipo machimo anunso adzakhululukidwa” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 6:37, nwtsty; w08 5/15 9-10 ¶13-14)
Luka 6:38—Tizikhala ndi chizolowezi chogawira ena zinthu (“Khalani opatsa” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 6:38, nwtsty)
Luka 6:38—Muyezo umene tikuyezera ena, iwonso adzatiyezera womwewo (“m’matumba anu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 6:38, nwtsty)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Luka 6:12, 13—Kodi Akhristu amene akufuna kupanga zosankha zikuluzikulu angatsanzire bwanji Yesu? (w07 8/1 6 ¶1)
Luka 7:35—Kodi mawu a Yesu palembali angatithandize bwanji ngati ena akutinenera zoipa? (“zotsatira zake” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 7:35, nwtsty)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 7:36-50
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 198 ¶4-5
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Muzitsanzira Yehova Pokhala Owolowa Manja: (15 min.) Onerani vidiyoyi. Kenako kambiranani mafunso otsatirawa:
Kodi Yehova ndi Yesu amasonyeza bwanji kuti ndi owolowa manja?
Kodi Yehova amatidalitsa bwanji tikakhala owolowa manja?
Kodi tingasonyeze bwanji kuti ndife owolowa manja pa nkhani yokhululukira ena?
Kodi tingasonyeze bwanji kuti ndife owolowa manja pa nkhani ya mmene timagwiritsira ntchito nthawi yathu?
Kodi tingasonyeze bwanji kuwolowa manja pa nkhani yoyamikira ena?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 21 ¶1-7 komanso tsamba 220-221
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 57 ndi Pemphero