Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 October tsamba 7
  • October 29–November 4

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 29–November 4
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 October tsamba 7

October 29–November 4

YOHANE 18-19

  • Nyimbo Na. 54 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yesu Anachitira Umboni Choonadi”: (10 min.)

    • Yoh. 18:36​—Choonadi chimafotokoza kwambiri za Ufumu wa Mesiya

    • Yoh. 18:37​—Yesu anachitira umboni choonadi chokhudza zolinga za Mulungu (“kudzachitira umboni,” “choonadi” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 18:37, nwtsty)

    • Yoh. 18:38a​—Pilato anatsutsa mfundo yoti padzikoli pangapezeke choonadi (“Choonadi n’chiyani?” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 18:38a, nwtsty)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yoh. 19:30​—Kodi mawu akuti Yesu ‘anapereka mzimu wake’ amatanthauza chiyani? (“kupereka mzimu wake” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 19:30, nwtsty)

    • Yoh. 19:31​—Kodi pali umboni wotani womwe umasonyeza kuti Yesu anaphedwa pa Nisani 14 mu 33 C.E? (“Sabata la tsiku limeneli linali lalikulu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 19:31, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yoh. 18:1-14

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. Kenako musonyezeni webusaiti yathu ya jw.org.

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse komanso funso limene mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 14 ¶6-7

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 46

  • “Akhristu Oona Amadziwika Chifukwa cha Chikondi​—Muzisangalala ndi Choonadi”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti ‘Muzikondana’​—Muzisangalala ndi Choonadi, Osati ndi Zosalungama. Ngati nthawi ilipo kambiranani mfundo za m’kabokosi kakuti “Chitsanzo cha M’Baibulo Chofunika Kuchiganizira.”

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 11

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 53 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena