Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 December tsamba 2
  • Munthu Amene Ankazunza Akhristu Anakhala Mkhristu Wakhama

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Munthu Amene Ankazunza Akhristu Anakhala Mkhristu Wakhama
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Kulalikira kwa Saulo Kunamudanitsa ndi Anthu
    Nsanja ya Olonda—2005
  • Wozunza Aona Kuunika Kwakukulu
    Nsanja ya Olonda—2000
  • Yesu Anasankha Saulo
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Mpingo “Unayamba Kukhala Pamtendere”
    ‘Kuchitira Umboni Mokwanira za Ufumu wa Mulungu’
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 December tsamba 2
Saulo wagwa pansi ataona kuwala kochokera kumwamba

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 9-11

Munthu Amene Ankazunza Akhristu Anakhala Mkhristu Wakhama

9:15, 16, 20-22

Saulo sanachedwe kukhala Mkhristu mogwirizana ndi zimene ankaphunzira. N’chiyani chinathandiza Saulo kusintha mwachangu chonchi pomwe ena zinkawavuta? Chifukwa choti ankaopa kwambiri Mulungu osati anthu ndiponso ankayamikira chifundo chimene Khristu anamusonyeza. Ngati mukuphunzira Baibulo koma simunabatizidwe, kodi mungakonde kutsanzira Saulo n’kuyamba kuchita mogwirizana ndi zimene mwaphunzira?

KODI MUKUDZIWA?

Aroma ankalola Ayuda kuti aziweruza okha milandu. Komanso Khoti Lalikulu la Ayuda ndiponso mkulu wa ansembe ankakhala ndi mphamvu zopereka chiweruzo kwa Ayuda omwe ankakhala kulikonse. Choncho iwo anali ndi mphamvu zopereka chilolezo kwa Saulo kuti akamange anthu onse omwe anakhala Akhristu, ngakhalenso amene ankakhala m’madera akutali kwambiri ngati ku Damasiko.

Mapu osonyeza Damasiko ndi Yerusalemu
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena