Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 March tsamba 6
  • March 25-31

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 25-31
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 March tsamba 6

March 25-31

1 AKORINTO 4-6

  • Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Chofufumitsa Chaching’ono Chimafufumitsa Mtanda Wonse”: (10 min.)

    • 1 Akor. 5:1, 2​—Mpingo wa ku Korinto unkalekerera munthu wina yemwe ankachita zoipa

    • 1 Akor. 5:5-8, 13​—Paulo anauza akulu kuti achotse “chofufumitsa” popereka munthuyo kwa Satana (it-2 230, 869-870)

    • 1 Akor. 5:9-11​—Anthu a mumpingo sayenera kumachezabe ndi munthu yemwe sakufuna kulapa (lvs 241, Mawu Akumapeto “Kuchotsa Munthu Mumpingo”)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • 1 Akor. 4:9​—Kodi atumiki a Mulungu a padziko lapansi amakhala bwanji ngati “choonetsedwa m’bwalo la masewera” kwa angelo? (w09 5/15 24 ¶16)

    • 1 Akor. 6:3​—Kodi Paulo ankatanthauza chiyani pamene analemba kuti: “Tidzaweruza angelo”? (it-2 211)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 1 Akor. 6:1-14 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 11)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) lvs 44 (th phunziro 3)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 78

  • “Muzigwiritsa Ntchito Mavidiyo Pophunzira ndi Anthu”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani ndi kukambirana vidiyo yosonyeza wofalitsa akugwiritsa ntchito vidiyo ya phunziro 4 m’kabuku ka Uthenga Wabwino.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 31

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 139 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena