Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 April tsamba 7
  • April 29–May 5

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 29–May 5
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 April tsamba 7

April 29–May 5

2 AKORINTO 1-3

  • Nyimbo Na. 44 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova ndi ‘Mulungu Amene Amatitonthoza M’njira Iliyonse’”: (10 min.)

    • [Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Akorinto.]

    • 2 Akor. 1:3​—Yehova ndi “Tate wachifundo chachikulu” (w17.07 13 ¶4)

    • 2 Akor. 1:4​—Timatha kutonthoza ena chifukwa ifenso timatonthozedwa ndi Yehova (w17.07 15 ¶14)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • 2 Akor. 1:22​—Kodi odzozedwa amalandira bwanji “chikole” kuchokera kwa mulungu, nanga amadindidwa bwanji “chidindo”? (w16.04 32)

    • 2 Akor. 2:14-16​—Kodi Paulo ayenera kuti ankaganizira za chiyani pamene ananena za “chionetsero chonyadirira kupambana”? (w10 8/1 23)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 2 Akor. 3:1-18 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 6)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) bhs 52-53 ¶3-4 (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 86

  • “Dziperekeni Kuti Muphunzitsidwe ndi Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani ndi kukambirana vidiyo yakuti Tinapeza Madalitso Ambiri Chifukwa Chophunzitsidwa ndi Yehova.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 35 ¶12-19

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 121 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena