July 15-21
2 ATESALONIKA 1-3
Nyimbo Na. 67 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Wosamvera Malamulo Adzaonekera”: (10 min.)
[Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Atesalonika.]
2 Ates. 2:6-8—‘Wosamvera malamulo,’ yemwe ankasocheretsa anthu, anali woti adzaonekera (it-1 972-973)
2 Ates. 2:9-12—Anthu omwe asocheretsedwa ndi ‘wosamvera malamulo’ adzaweruzidwa (it-2 245 ¶7)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
2 Ates. 1:7, 8—Kodi Baibulo limatanthauza chiyani likamanena kuti Yesu ndi angelo ake adzaonekera “m’moto walawilawi”? (it-1 834 ¶5)
2 Ates. 2:2—Kodi m’vesili, Paulo ankatanthauza chiyani ponena kuti “mawu ouziridwa”? (it-1 1206 ¶4)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 2 Ates. 1:1-12 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. (th phunziro 6)
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba, kenako musonyezeni buku la Zimene Baibulo Limaphunzitsa. (th phunziro 12)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Kodi Utumiki Wanu Mumangouchita Mwamwambo Chabe?: (15 min.) Onerani vidiyo yakuti, Muziikirapo Mtima pa Utumiki Wanu.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 43 ndime 8-18
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 64 ndi Pemphero