Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 August tsamba 2
  • August 5-11

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 5-11
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 August tsamba 2

August 5-11

2 Timoteyo 1-4

  • Nyimbo Na. 150 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mulungu Sanatipatse Mzimu Wamantha”: (10 min.)

    • [Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Timoteyo.]

    • 2 Tim. 1:7​—Muziyesetsa kukhala ‘oganiza bwino’ mukakumana ndi mayesero (w09 5/15 15 ¶9)

    • 2 Tim. 1:8​—Musamachite manyazi ndi uthenga wabwino (w03 3/1 9 ¶7)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • 2 Tim. 2:3, 4​—Kodi tingatani kuti tisamachite nawo kwambiri “zamalonda zimene anthu wamba amachita”? (w17.07 10 ¶13)

    • 2 Tim. 2:23​—Kodi tingakane bwanji “mafunso opusa ndi opanda nzeru”? (w14 7/15 14 ¶10)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 2 Tim. 1:1-18 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Mafanizo Abwino, kenako kambiranani phunziro 8 m’kabuku ka Kuphunzitsa.

  • Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w14 7/15 13 ¶3-7​—Mutu: Kodi Anthu a Yehova Amakana Bwanji “Kuchita Zosalungama”? (th phunziro 7)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 85

  • “Muzicheza ndi Anthu Amene Amakonda Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Muzipewa Kugwirizana ndi Anthu a Makhalidwe Oipa.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 45

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 55 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena