Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 March tsamba 5
  • March 23-29

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 23-29
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 March tsamba 5

March 23-29

GENESIS 27-28

  • Nyimbo Na. 10 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yakobo Analandira Madalitso”: (10 min.)

    • Ge 27:6-10​—Rabeka anathandiza Yakobo kuti alandire madalitso amene ankayenera kulandira (w04 4/15 11 ¶4-5)

    • Ge 27:18, 19​—Yakobo ananamizira kuti anali Esau pokaonekera kwa bambo ake (w07 10/1 31 ¶2-3)

    • Ge 27:27-29​—Isaki anadalitsa Yakobo ngati mwana wake woyamba kubadwa (it-1 341 ¶6)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Ge 27:46–28:2​—Kodi anthu apabanja angaphunzire chiyani kwa Isaki ndi Rabeka? (w06 4/15 6 ¶3-4)

    • Ge 28:12, 13​—Kodi loto la Yakobo lokhudza “makwerero” likusonyeza chiyani? (w04 1/15 28 ¶6)

    • Kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ge 27:1-23 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi, kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi wofalitsayu anasonyeza bwanji kuti amamvetsera pamene mwininyumba amafotokoza maganizo ake? Kodi wofalitsayu anagwiritsa ntchito bwanji zinthu zomwe timagwiritsa ntchito pophunzitsa?

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 6)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) jl phunziro 17 (th phunziro 11)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 34

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 78

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (Osapitirira 3 min.)

  • Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena