September 21-27
EKISODO 27-28
Nyimbo Na. 25 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Zovala za Ansembe?” (10 min.)
Eks 28:30—Tiyenera kufufuza zimene Yehova amafuna kuti tizichita (it-2 1143)
Eks 28:36—Tiyenera kukhala oyera (it-1 849 ¶3)
Eks 28:42, 43—Tizichita zinthu mwaulemu tikamalambira Yehova (w08 8/15 15 ¶17)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Eks 28:15-21—Kodi miyala yamtengo wapatali yomwe inali pachovala chapachifuwa cha mkulu wa ansembe wa ku Isiraeli iyenera kuti inachokera kuti? (w12 8/1 26 ¶1-3)
Eks 28:38—Kodi “zinthu zopatulika” zinali chiyani? (it-1 1130 ¶2)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Eks 27:1-21 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako musiyireni khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 1)
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 2)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min) lvs 111 ¶20-21 (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Kulalikira Tili pa Kamera Kapena Pogwiritsa Ntchito Intakomu”: (15 min.) Nkhani Yokambirana. Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyo yoyamba, kenako onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyo yachiwiri.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 101
Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)
Nyimbo Na. 56 ndi Pemphero