Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 October tsamba 4
  • October 12-18

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 12-18
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 October tsamba 4

October 12-18

EKISODO 33-34

  • Nyimbo Na. 115 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Makhalidwe Abwino Kwambiri a Yehova”: (10 min.)

    • Eks 34:5​—Kudziwa dzina la Mulungu kumatanthauza kudziwa zolinga zake, zochita zake komanso makhalidwe ake (it-2 466-467)

    • Eks 34:6​—Makhalidwe a Yehova amatichititsa kumukonda (w09 5/1 18 ¶3-5)

    • Eks 34:7​—Yehova amakhululukira anthu ochimwa amene alapa (w09 5/1 18 ¶6)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Eks 33:11, 20​—Kodi Mulungu analankhula ndi Mose “pamasom’pamaso” m’njira iti? (w04 3/15 27 ¶5)

    • Eks 34:23, 24​—N’chifukwa chiyani amuna a ku Isiraeli ankafunika kukhala ndi chikhulupiriro kuti azipita kuzikondwerero zitatu za pa chaka? (w98 9/1 20 ¶5)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Eks 33:1-16 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi, kenako funsani mafunso otsatirawa: Kodi wofalitsa anathandiza bwanji mwininyumba kuti amvetse mfundo yamulembalo? Nanga anathandiza bwanji mwininyumba kuti aganizire mfundoyo?

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 16)

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Musonyezeni buku la Zimene Baibulo Limaphunzitsa n’kuyamba kuphunzira naye mutu 2. (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 80

  • “Achinyamata, Kodi Yehova Ndi Mnzanu Wapamtima?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Achinyamata​—“Talawani Ndipo Muona Kuti Yehova Ndi Wabwino.”

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 104

  • Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)

  • Nyimbo Na. 2 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena