Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 November tsamba 5
  • November 23-29

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 23-29
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 November tsamba 5

NOVEMBER 23-29

LEVITIKO 6-7

  • Nyimbo Na. 46 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Nsembe Yosonyeza Kuyamikira”: (10 min.)

    • Le 7:11, 12​—Anthu ankapereka nsembe ina yachiyanjano mwa kufuna kwawo posonyeza kuyamikira (w19.11 22 ¶9)

    • Le 7:13-15​—Zinali ngati munthu amene akupereka nsembe yachiyanjanoyo komanso banja lake akudyera limodzi ndi Yehova posonyeza kuti ali naye pa mtendere (w00 8/15 15 ¶15)

    • Le 7:20​—Anthu oyera okha ndi amene akanatha kupereka nsembe yachiyanjano yovomerezeka (w00 8/15 19 ¶8)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Le 6:13​—Kodi Ayuda amakhulupirira kuti moto wapaguwa lansembe unayatsidwa bwanji, nanga Malemba amasonyeza chiyani? (it-1 833 ¶1)

    • Le 6:25​—Kodi nsembe zamachimo zinkasiyana bwanji ndi nsembe zopsereza komanso zachiyanjano? (si 27 ¶15)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Le 6:1-18 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako tchulani mfundo inayake yam’magazini yogawira ya Nsanja ya Olonda Na. 2 2020, ndipo perekani magaziniyo. (th phunziro 3)

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako musonyezeni webusaiti yathu ya jw.org n’kumupatsa khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 11)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) bhs 178-179 ¶12-13 (th phunziro 6)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 18

  • Khalani Bwenzi la Yehova​—Uzithokoza: (5 min.) Onerani vidiyoyi. Pemphani ana amene mwawasankhiratu, ngati n’zotheka, kuti abwere kupulatifomu kudzayankha mafunso okhudza vidiyoyo.

  • Zofunika Pampingo: (10 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 110

  • Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)

  • Nyimbo Na. 30 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena