Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsamba 4
  • March 15-21

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 15-21
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 March tsamba 4

March 15-21

NUMERI 11-12

  • Nyimbo Na. 46 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupewa Mtima Wodandaula?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Nu 11:7, 8​—Kodi mmene mana ankaonekera komanso mmene ankakomera zinkasonyeza bwanji kuti Yehova ndi wabwino? (it-2 309)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 11:1-15 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuitanira Anthu ku Chikumbutso: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha zimene tinganene poitanira anthu ku Chikumbutso. Pambuyo poti mwininyumba wasonyeza chidwi, yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, Tizikumbukira Imfa ya Yesu kenako kambiranani naye mfundo za m’vidiyoyi. (th phunziro 11)

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Pangani ulendo wobwereza kwa munthu amene anasonyeza chidwi ndipo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. (th phunziro 4)

  • Ulendo Wobwereza: (5 min.) Pambuyo pa nkhani ya Chikumbutso, yambani kukambirana ndi munthu wachidwi amene anabwera ndipo muyankhe funso limene wafunsa lokhudza mwambowo. (th phunziro 2)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 19

  • “Kodi Mukukonzekera Chikumbutso?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Lengezani zilengezo zilizonse zimene zingakhalepo zokhudza Chikumbutso. Onerani vidiyo yakuti, Mmene Mungapangire Mkate wa Chikumbutso.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 125

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 129 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena