Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsamba 2
  • May 3-9

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 3-9
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 May tsamba 2

May 3-9

NUMERI 27-29

  • Nyimbo Na. 106 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzitsanzira Yehova Yemwe Ndi Wosakondera”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Nu 28:7, 14​—Kodi nsembe zachakumwa zinali chiyani? (it-2 528 ¶5)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Nu 28:11-31 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Cholinga cha Mulungu​—Ge 1:28. Muziimitsa nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali m’vidiyoyi.

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 4)

  • Nkhani: (5 min.) w07 4/1 17-18​—Mutu: Kodi N’chiyani Chimachititsa Kuti Yehova Azisangalala Ndi Nsembe Zathu? (th phunziro 16)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 82

  • Khalani Bwenzi la Yehova​—Uzikonda Mnzako: (6 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako ngati n’zotheka, funsani ana omwe munawasankhiratu mafunso awa: N’chifukwa chiyani ana ena sankafuna kuchita zinthu ndi Priya kusukulu? Kodi Sofiya anasonyeza bwanji chikondi kwa Priya? Kodi mungasonyeze bwanji chikondi kwa anthu omwe ndi osiyana ndi inu?

  • Kodi Mnzako Weniweni Ungamudziwe Bwanji?: (9 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yamakatuniyi. Kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi muyenera kuyang’ana zinthu ziti mukamasankha anzanu? Kodi anzanu abwino mungawapeze kuti? Kodi mungatani kuti ubwenzi wanu uziyenda bwino?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 132 ndi bokosi lakuti “Mpachikeni”

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 20 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena