Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsamba 12
  • June 14-20

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • June 14-20
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 May tsamba 12

June 14-20

DEUTERONOMO 5-6

  • Nyimbo Na. 134 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Phunzitsani Ana Anu Kuti Azikonda Yehova”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • De 5:21​—Kodi lamulo loletsa kusirira kwa nsanje limatiphunzitsa chiyani? (w19.02 22 ¶11)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 5:1-21 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. M’pempheni kuti muziphunzira naye Baibulo ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (th phunziro 9)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Sinthani ulaliki wanu kuti ugwirizane ndi nkhani imene mwininyumba watchula, ndipo werengani lemba logwirizana ndi nkhaniyo. (th phunziro 12)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) fg phunziro 9 ¶6-7 (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 105

  • “Muzisonyeza Chikondi M’banja”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzisonyeza Chikondi Chosatha M’banja.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 138

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 22 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena