Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsamba 8
  • August 2-8

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 2-8
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 July tsamba 8

AUGUST 2-8

DEUTERONOMO 22-23

  • Nyimbo Na. 1 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Zinyama?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • De 23:19, 20—N’chifukwa chiyani mlendo akatenga ngongole ankafunika kupereka chiwongoladzanja pomwe Mwisiraeli sankafunika kupereka chiwongoladzanja? (it-1 600)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 23:1-14 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • “Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki—Muziwafika Pamtima”: (9 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muziwonjezera Luso Lanu Kuti Muzisangalala ndi Ntchito Yophunzitsa—Muziwafika Pamtima.

  • Nkhani: (5 min.) g 4/15 13—Mutu: Kodi Kupha Nyama N’kulakwa? (th phunziro 14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 62

  • Zofunika Pampingo: (15 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 2 ndime 17-21, Mfundo za M’Baibulo tsa. 27-30, Mawu Akumapeto 7

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 124 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena