AUGUST 9-15
DEUTERONOMO 24-26
Nyimbo Na. 137 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Akazi?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
De 24:1—N’chifukwa chiyani sitinganene kuti Chilamulo cha Mose chinkachititsa kuti mwamuna azithetsa ukwati mosavuta? (it-1 640 ¶5)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) De 26:4-19 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 1)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Gawirani chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 2)
Nkhani: (5 min.) w19.06 23-24 ¶13-16—Mutu: Kodi Tingalimbikitse Bwanji Munthu Amene Mwamuna Kapena Mkazi Wake Wamwalira? (th phunziro 20)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Uziona Akazi Achikulire Ngati Amayi Ako, Akazi Achitsikana Ngati Alongo Ako”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzisonyeza Chikondi Chosatha Mumpingo Wachikhristu—Muzikonda Akazi Amasiye ndi Ana Amasiye.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 3 ndime 1-7
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 57 ndi Pemphero