October 25-31
YOSWA 15-17
Nyimbo Na. 146 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muziteteza Cholowa Chanu Chomwe Ndi Chamtengo Wapatali”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yos 17:15, 18—Kodi tikudziwa bwanji kuti ku Isiraeli kunali mitengo yambiri? (w15 7/15 32)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yos 15:1-12 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Muitanireni kumisonkhano yathu. (th phunziro 19)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 4)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 01 mfundo 6 komanso Zimene Ena Amanena (th phunziro 9)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muzilalikira Uthenga Wabwino Wakuti Dziko Labwino Layandikira”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya nyimbo yakuti Dziko Latsopano Lomwe Likubwera.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 6 ndime 20-23, mfundo za m’Baibulo tsa. 86-88
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 94 ndi Pemphero