January 17-23
OWERUZA 20-21
Nyimbo Na. 47 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzifunsira Nzeru kwa Yehova”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Owe 20:16—Kodi kale gulaye ankagwiritsidwa ntchito bwanji pa nkhondo? (w14 5/1 11 ¶4-6)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Owe 20:1-13 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 5)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi a Mboni za Yehova ndi Anthu Otani? (th phunziro 17)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lffi phunziro 03 mawu oyamba komanso mfundo 1-3 (th phunziro 4)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Chilengedwe Chimatithandiza Kuti Tizidalira Kwambiri Nzeru za Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kodi Zinangochitika Zokha? Mmene Nyerere Zimapewera Kutchingirana Njira, komanso yakuti Kodi Zinangochitika Zokha? Mmene Njuchi Imaulukira. Limbikitsani omvera kuti pa kulambira kwa pabanja akakambirane nkhani za pa jw.org za mutu wakuti “Kodi Zinangochitika Zokha?”
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 10 ndime 19-24, mfundo za m’Baibulo tsa. 143-146
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 110 ndi Pemphero