Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsamba 15
  • February 28–March 6

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 28–March 6
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 January tsamba 15

February 28–March 6

1 SAMUELI 9-11

  • Nyimbo Na. 121 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Sauli Anali Wodzichepetsa Poyamba”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Sa 9:9​—Kodi n’kutheka kuti mawu a palembali ankatanthauza chiyani? (w05 3/15 22 ¶8)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 9:1-10 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • ““Zimene Mungachite Kuti Muzisangalala Kwambiri mu Utumiki​—Muzithandiza Ophunzira Baibulo Kuti Asamacheze ndi Anthu Olakwika”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Muzithandiza Amene Mukuphunzira Nawo Baibulo Kuti Asamacheze ndi Anthu Olakwika.

  • Nkhani: (5 min.) w15 4/15 6-7 ¶16-20​—Mutu: Mfundo Zomwe Zingathandize Pophunzitsa Ena. (th phunziro 19)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 37

  • Lipoti la Chaka Chautumiki: (15 min.) Nkhani yokambidwa ndi mkulu. Pambuyo powerenga chilengezo chochokera ku ofesi ya nthambi chokhudza lipoti la chaka chautumiki, funsani ofalitsa omwe munawasankhiratu kuti afotokoze zinthu zolimbikitsa zimene anakumana nazo mu utumiki chaka chathachi.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lvs mutu 12 ndime 15-22, mfundo za m’Baibulo tsa. 169-171

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 90 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena