Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsamba 3
  • May 9-15

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 9-15
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 May tsamba 3

May 9-15

1 SAMUELI 30-31

  • Nyimbo Na. 8 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Dzilimbitseni mwa Yehova Mulungu Wanu”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Sa 30:23, 24​—Kodi tikuphunzira chiyani pa nkhani imeneyi? (w05 3/15 24 ¶8)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Sa 30:1-10 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Wobwereza: Kuvutika​—1Yo 5:19. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.

  • Ulendo Wobwereza: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 8)

  • Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo yambani kuphunzira naye Baibulo mu phunziro 01. (th phunziro 16)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 43

  • Khalani Bwenzi la Yehova​—Muzipemphera Nthawi Iliyonse: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako ngati n’zotheka, funsani ana omwe munawasankhiratu mafunso awa: N’chifukwa chiyani tiyenera kupemphera kwa Yehova? Kodi ndi pa nthawi ziti pamene tiyenera kupemphera? Kodi ndi zinthu ziti zimene mungatchule m’pemphero?

  • Zofunika Pampingo: (10 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 03

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 95 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena