Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsamba 8
  • May 30–June 5

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 30–June 5
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 May tsamba 8

May 30–June 5

2 SAMUELI 7-8

  • Nyimbo Na. 22 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Anachita Pangano ndi Davide”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Sa 8:2​—Kodi mmene Davide anagonjetsera Amowabu zinakwaniritsa bwanji ulosi? (it-2 206 ¶2)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Sa 7:1-17 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba, kenako mugwirizanitse ndi zimene zikuchitika m’dera lanu. Mugawireni magazini yomwe ili ndi nkhani imene anatchula. (th phunziro 13)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza, kenako mugwirizanitse ndi zimene zikuchitika m’dera lanu. Mufotokozereni zokhudza phunziro la Baibulo la ulele, ndipo m’patseni khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 18)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 04 zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 91

  • Zofunika Pampingo: (10 min.)

  • “Muzigwiritsa Ntchito Zimene Zikuchitika M’dera Lanu Mukakhala mu Utumiki”: (5 min.) Nkhani yokambirana.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 06

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Yatsopano ya Msonkhano wa 2022 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena