Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsamba 7
  • July 25-31

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • July 25-31
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 July tsamba 7

July 25-31

2 SAMUELI 23-24

  • Nyimbo Na. 76 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mumapereka Nsembe?”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Sa 23:15-17​—N’chifukwa chiyani Davide anakana kumwa madzi? (w05 5/15 19 ¶6)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Sa 23:1-12 (th phunziro 11)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani kukambirana pogwiritsa ntchito tsamba lomaliza la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. Konzani zoti mudzabwerenso kuti mudzakambirane phunziro 01 n’kupeza yankho la funso lake. (th phunziro 9)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Pitani kwa munthu amene analandira kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo musonyezeni mmene phunziro la Baibulo limachitikira. (th phunziro 3)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 05 zomwe taphunzira, kubwereza, komanso zolinga (th phunziro 19)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 17

  • Muzipereka Nsembe Mofunitsitsa (Sl 54:6): (9 min.) Onerani vidiyoyi.

  • Khalani Bwenzi la Yehova​—Kudzimana: (6 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani ana omwe munawasankhiratu mafunso awa: Kodi Kalebe ndi Sofiya anadzimana chiyani? Kodi chitsanzo cha Yesu chinathandiza bwanji Kalebe? Kodi inuyo mwadzimana zinthu ziti chifukwa cha Yehova komanso anthu ena?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 13 ndi mawu akumapeto 1

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 32 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena