August 15-21
1 MAFUMU 5-6
Nyimbo Na. 122 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Anagwira Ntchito Mwamphamvu Komanso ndi Mtima Wonse”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Mf 6:1—Kodi vesili likunena zotani zokhudza Baibulo? (g 5/12 17, bokosi)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mf 5:1-12 (th phunziro 12)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani kukambirana pogwiritsa ntchito tsamba lomaliza la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. Konzani zoti mudzakumanenso kuti mudzayankhe funso lomwe ndi mutu wa phunziro 01. (th phunziro 11)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Pitani kwa munthu amene analandira kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo musonyezeni mmene phunziro la Baibulo limachitikira. (th phunziro 2)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 06 mfundo 5 (th phunziro 9)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Tinaona Dzanja la Yehova Pamene Tinkamanga Nyumba za Ufumu: (15 min.) Onerani vidiyoyi. Kenako funsani mafunso otsatirawa: N’chiyani chikusonyeza kuti Yehova anadalitsa ntchito yomanga Nyumba za Ufumu ku Micronesia? Kodi mzimu woyera umathandiza bwanji pomanga malo olambirira? Kodi munaona kuti Yehova anadalitsa bwanji ntchito zomanga zimene munagwira nawo?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 16
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 20 ndi Pemphero