Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsamba 12
  • August 22-28

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 22-28
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 July tsamba 12

August 22-28

1 MAFUMU 7

  • Nyimbo Na. 7 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Tikuphunzira Chiyani pa Zipilala Ziwiri”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 1Mf 7:23​—Kodi tikuphunzira chiyani pa “thanki yamkuwa” yaikulu imene inamangidwa pakachisi? (it-1 263)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mf 7:1-12 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 6)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo musonyezeni mmene phunziro la Baibulo limachitikira. (th phunziro 3)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 06 mfundo 6 komanso Zimene Ena Amanena (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 72

  • Zofunika Pampingo: (5 min.)

  • “Ntchito Yapadera Yoyambitsa Maphunziro a Baibulo mu September”: (10 min.) Nkhani yokambirana yokambidwa ndi woyang’anira utumiki. Onerani vidiyo ya Ulendo Woyamba: Phunziro la Baibulo​—Sl 37:29. Fotokozani zimene mpingo wanu wakonza zokhudza ntchito yapaderayi.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 17

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 13 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena