August 29–September 4
1 MAFUMU 8
Nyimbo Na. 41 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Solomo Anapemphera Modzichepetsa Komanso Mochokera Pansi pa Mtima”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Mf 8:27—Kodi mawu amene Solomo anayankhulawa satanthauza chiyani? (it-1 1060 ¶4)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mf 8:31-43 (th phunziro 12)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 1)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Kenako mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? (th phunziro 15)
Nkhani: (5 min.) km 5/10 2—Mutu: Atumiki a Chikhristu Ayenera Kupemphera. (th phunziro 14)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kodi Mumayesetsa Kuona Mmene Yehova Akuyankhira Mapemphero Anu?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Yehova Ndi “Wakumva Pemphero.”
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 18 mfundo 1-5
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 107 ndi Pemphero