September 19-25
1 MAFUMU 13-14
Nyimbo Na. 21 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kukhala Okhutira Komanso Odzichepetsa?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Mf 14:13—Kodi lembali likutiphunzitsa chiyani zokhudza Yehova? (w10 7/1 29 ¶5)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mf 13:1-10 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha zimene tinganene pa ntchito yapadera yoyambitsa maphunziro a Baibulo. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 7)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Pitirizani phunziro la Baibulo lomwe munayambitsa pa ulendo woyamba, pogwiritsa ntchito phunziro 01 la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 9)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 07 mfundo 5 (th phunziro 19)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muzidalira Yehova Mukakumana ndi Mavuto Azachuma”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Mangani Nyumba Yolimba—‘Muzikhala Okhutira Ndi Zimene Muli Nazo.’
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 19 mfundo 5-6, zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 56 ndi Pemphero