October 3-9
1 MAFUMU 17-18
Nyimbo Na. 32 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mukayikakayika Mpaka Liti?”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Mf 18:1—N’chifukwa chiyani Yesu ananena kuti chilala cha m’nthawi ya Eliya chinatenga “zaka zitatu ndi miyezi 6”? (Lu 4:25; w08 4/1 19, bokosi)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mf 18:36-46 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Woyamba: Baibulo—2Ti 3:16, 17. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 12)
Nkhani: (5 min.) w14 2/15 14-15—Mutu: Kodi Tingaphunzire Chiyani pa Chikhulupiriro cha Mkazi Wamasiye? (th phunziro 13)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 21
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 83 ndi Pemphero