October 10-16
1 MAFUMU 19-20
Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Tizidalira Yehova Kuti Atilimbikitse”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Mf 19:19-21—Kodi nkhaniyi ikutiphunzitsa chiyani zokhudza kulandira utumiki watsopano wopatulika? (w97 11/1 31 ¶1
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mf 19:1-14 (th phunziro 12)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo ya Ulendo Wobwereza: Baibulo—Yob 26:7. Muziimitsa vidiyoyi nthawi iliyonse imene pali chizindikiro chosonyeza kuti muime n’kufunsa omvera mafunso omwe ali muvidiyoyi.
Ulendo Wobwereza: (3 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. (th phunziro 18)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 07 mfundo 7 komanso Zimene Ena Amanena (th phunziro 7)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Pitirizani Kuona Zinthu Moyenera: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera mafunso awa: Kodi ndi mfundo za m’Baibulo ziti zimene zingatithandize kuti tizionabe zinthu moyenera? Kodi Yehova analimbikitsa bwanji Eliya? Kodi Yehova amatilimbikitsa komanso amatisamalira bwanji?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 22
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 57 ndi Pemphero