Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 5
  • November 21-27

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 21-27
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 5

November 21-27

2 MAFUMU 9-10

  • Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Anachita Zinthu Molimba Mtima, Modzipereka Komanso Mofunitsitsa”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mf 10:29, 31​—Kodi tingaphunzire chiyani kuchokera pa zimene Yehu analakwitsa? (w11 11/15 5 ¶6-7)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 9:1-14 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 1)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muuzeni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu kwaulere, kenako mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 12)

  • Nkhani: (5 min.) w13 5/15 8-9 ¶3-6​—Mutu: Tsanzirani Yehova ndi Yesu pa Nkhani ya Kudzipereka. (th phunziro 16)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 64

  • Zimene Achinyamata Anzanu Amanena​—Kuzengereza: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi. Kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: Kodi n’chiyani chingachititse munthu kuchita zinthu mozengereza? N’chifukwa chiyani timasangalala tikakhala kuti sitinachite zinthu mozengereza?

  • “Zimene Zingatithandize Kuti Tisamazengereze Pochita Zinthu”: (10 min.) Nkhani yokambirana.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 28

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 19 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena