Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 12
  • December 19-25

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 19-25
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 12

December 19-25

2 MAFUMU 18-19

  • Nyimbo Na. 148 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zimene Adani Athu Amachita Pofuna Kutifooketsa”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mf 19:37​—Kodi lembali likusonyeza bwanji kufunika kokhala osamala kwambiri tikafuna kudalira zimene ofukula zinthu zakale anapeza? (it-1 155 ¶4)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 18:1-12 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Muitanireni ku misonkhano yathu, ndipo yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani? kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 1)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene muli mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Muuzeni kuti timaphunzira Baibulo ndi anthu kwaulere ndipo musiyireni khadi lodziwitsa anthu za phunziro la Baibulo. (th phunziro 2)

  • Nkhani: (5 min.) w20.11 15 ¶14​—Mutu: Kodi Tingapempherere Bwanji Anthu Amene Akuzunzidwa? (th phunziro 14)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 128

  • “Muzisangalala Mukamazunzidwa”: (8 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Tikhoza Kumasangalalabe Ngakhale Kuti Tikuzunzidwa.

  • Zofunika Pampingo: (7 min.)

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 32 mfundo 1-4 ndi bokosi lakuti “Kugwirizana kwa Maloto a Mtengo ndi Ufumu wa Mulungu”

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 22 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena