Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 14
  • December 26–January 1

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • December 26–January 1
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 14

December 26–January 1

2 MAFUMU 20–21

  • Nyimbo Na. 41 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Pemphero Linachititsa Yehova Kuchitapo Kanthu”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • 2Mf 21:13​—Kodi Yehova anayeza Yerusalemu ndi thabwa lowongolera m’njira yotani? (it-2 240 ¶1)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 2Mf 21:1-15 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 4)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mufotokozereni za webusaiti yathu ya jw.org, ndipo mugawireni khadi lodziwitsa anthu za webusaitiyi. (th phunziro 6)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 08 mfundo 6 (th phunziro 19)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 47

  • “Mapemphero Athu ndi Amtengo Wapatali kwa Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ndimakonda Kupemphera.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 32 mfundo 5-6, zomwe taphunzira, kubwereza komanso zolinga

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 142 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena