Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsamba 10
  • October 16-22

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • October 16-22
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 September tsamba 10

October 16-22

YOBU 6-7

  • Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Moyo Ukafika Povuta”: (10 min.)

  • Mfundo Zothandiza: (10 min.)

    • Yob 6:29—N’chiyani chingatithandize kuti tipewe kuweruza molakwika abale athu? (w20.04 16 ¶10)

    • Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?

  • Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 6:​1-21 (th phunziro 2)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 7)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 11)

  • Nkhani: (5 min.) w22.01 12-13 ¶15-18—Mutu: Tiziphunzitsa Mogwira Mtima Ngati Yakobo —Tizigwiritsa Ntchito Mafanizo Ogwira Mtima. (th phunziro 8)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 144

  • “Yehova Amapulumutsa Anthu Odzimvera Chisoni”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff kubwereza gawo 4

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 143 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena