Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb24 January tsamba 2
  • January 1-7

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • January 1-7
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
mwb24 January tsamba 2

JANUARY 1-7

YOBU 32-33

Nyimbo Na. 102 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

[Chithunzi chapachikuto]Elihu akumvetsera mwatcheru kwa Yobu, amene ali ndi zilonda thupi lonse.

Elihu akumvetsera mwatcheru pamene Yobu akufotokoza mavuto ake

1. Muzilimbikitsa Amene Akulimbana ndi Nkhawa

(10 min.)

Mukamachita zinthu ndi ena muziwaona kuti ndi anzanu (Yob 33:1; it-1 710)

Muzikhala achifundo ndipo musamawaweruze (Yob 33:6, 7; w14 6/15 25 ¶8-10)

Musanalankhule, muzimvetsera n’kuganizira ngati mmene anachitira Elihu (Yob 33:8-12, 17; w20.03 23 ¶17-18; Onani chithunzi chapachikuto)

Mlongo akumvetsera mwatcheru pamene mlongo wina amene akulera yekha ana akufotokoza nkhawa zake. Ana awiri a mayiyu akusewera m’chipinda china.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Yob 33:25—Kodi lembali likutithandiza bwanji kuti pamene tikukalamba tisamadere nkhawa za mmene tikuonekera? (w13 1/15 19 ¶10)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Yob 32:1-22 (th phunziro 12)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Kuchita Chidwi ndi Anthu—Zomwe Yesu Anachita

(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani kabuku ka lmd phunziro 1 mfundo 1-2.

5. Kuchita Chidwi ndi Anthu—Zomwe Mungachite Potsanzira Yesu

(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 1 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 116

6. Zofunika Pampingo

(15 min.)

7. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 4 bokosi patsamba 30

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 54 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena