Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb24 November tsamba 3
  • November 11-17

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • November 11-17
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
mwb24 November tsamba 3

NOVEMBER 11-17

SALIMO 106

Nyimbo Na. 36 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

1. “Iwo Anaiwala Mulungu, Mpulumutsi Wawo”

(10 min.)

Aisiraeli atayamba kuchita mantha, anapandukira Yehova (Eks 14:11, 12; Sl 106:7-9)

Aisiraeli atamva njala komanso ludzu, anayamba kung’ung’udzira Yehova (Eks 15:24; 16:3, 8; 17:2, 3; Sl 106:13, 14)

Pamene Aisiraeli anali ndi nkhawa, anayamba kulambira mafano (Eks 32:1; Sl 106:19-21; w18.07 20 ¶13)

Mlongo akukonzekera kulowa mu utumiki, ndipo akuganizira mmene Yehova wakhala akumuthandizira m’mbuyomu. Zithunzi: 1. Abale awiri akucheza naye pa ulendo waubusa. 2. Walandira chikwama chomwe muli zakudya. 3. Walandira kalata komanso chithunzi kuchokera kwa mnzake.

FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi kuganizira mmene Yehova wakhala akutithandizira m’mbuyomu, kungatithandize bwanji pamene takumana ndi mavuto?

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 106:36, 37—Kodi pali kugwirizana kotani pakati pa kulambira mafano ndi kupereka nsembe kwa ziwanda? (w06 7/15 13 ¶9)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Sl 106:21-48 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Kuphunzitsa M’njira Yosavuta—Zomwe Yesu Anachita

(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani kabuku ka lmd phunziro 11 mfundo 1-2.

5. Kuphunzitsa M’njira Yosavuta—Zomwe Mungachite Potsanzira Yesu

(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 11 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 78

6. Zofunika Pampingo

(15 min.)

7. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 18 ¶1-5, bokosi patsamba 142, 144

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 77 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena